Since 1971, ADMARC has been at the forefront of agricultural development in Malawi, connecting smallholder farmers and traders to local and international markets. With 11 divisional offices and over 240 markets nationwide, ADMARC plays a pivotal role in buying and selling agricultural commodities, including maize, tobacco, cotton, and groundnuts.
Operating key facilities such as cotton ginneries, processing plants, and depots across the country, ADMARC ensures the smooth flow of agricultural trade. Our mission is to empower farmers, drive economic growth, and support Malawi’s agricultural sector through strategic marketing and commodity trading.
Kuyambira m’chaka cha 1971, ADMARC yakhala patsogolo pa chitukuko cha ulimi m’Malawi, kulumikiza alimi ang’onoang’ono ndi amalonda kumisika ya m’dziko muno ndi yakunja. Pokhala ndi ma ofesi a mzigawo 11 ndi misika yopitilira 240 mdziko lonse, ADMARC ili ndi gawo lalikulu pakugula ndi kugulitsa zinthu zaulimi monga chimanga, fodya, thonje ndi mtedza.
Bungwe la ADMARC limaonetsetsa kuti malonda a zaulimi akuyenda bwino m’dziko la Malawi pogwiritsa ntchito zipangizo zamakono monga malo opangira thonje, zigayo, ndi malo osungiramo katundu. Cholinga chathu ndi kupatsa mphamvu alimi, kulimbikitsa chuma, komanso kuthandizira ulimi mMalawi kudzera mu úkadaulo wa za malonda.